-
Genesis 31:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno Labani anafunsa Yakobo kuti: “Nʼchiyani wachitachi? Nʼchifukwa chiyani wandipusitsa nʼkutenga ana anga aakazi ngati akapolo ogwidwa kunkhondo?
-