Genesis 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu anapatsa mtundawo dzina lakuti Dziko,+ koma madziwo anawapatsa dzina lakuti Nyanja.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.+
10 Mulungu anapatsa mtundawo dzina lakuti Dziko,+ koma madziwo anawapatsa dzina lakuti Nyanja.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.+