Genesis 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ndiwe wotembereredwa, ndipo ndikukuthamangitsa mʼdera limene nthaka yake yatsegula pakamwa nʼkulandira magazi a mʼbale wako, amene iwe wakhetsa ndi manja ako.+
11 Tsopano ndiwe wotembereredwa, ndipo ndikukuthamangitsa mʼdera limene nthaka yake yatsegula pakamwa nʼkulandira magazi a mʼbale wako, amene iwe wakhetsa ndi manja ako.+