-
Genesis 31:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Nʼchifukwa chiyani unachoka mozemba osandiuza? Ukanandiuza ndikanatsanzikana nawe mosangalala, tikuimba nyimbo, maseche ndi azeze.
-