Genesis 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikanatha kukuchitirani zoipa, koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.’+
29 Ndikanatha kukuchitirani zoipa, koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.’+