-
Genesis 31:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Rakele anali atatenga aterafi aja nʼkuwabisa mʼchishalo choika pangamila, nʼkuchikhalira. Labani anafunafuna mutenti monsemo koma sanawapeze aterafiwo.
-