Genesis 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako Rakele anauza bambo ake kuti: “Musandikwiyire mbuyanga chifukwa sinditha kunyamuka pano. Kungoti sindili bwino malinga ndi chikhalidwe chathu akazife.”+ Labani anapitiriza kufunafuna mosamala koma sanawapeze aterafiwo.+
35 Kenako Rakele anauza bambo ake kuti: “Musandikwiyire mbuyanga chifukwa sinditha kunyamuka pano. Kungoti sindili bwino malinga ndi chikhalidwe chathu akazife.”+ Labani anapitiriza kufunafuna mosamala koma sanawapeze aterafiwo.+