-
Genesis 31:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno Yakobo anapsa mtima nʼkuyamba kukalipira Labani. Iye anafunsa Labani kuti: “Kodi ndakulakwirani chiyani? Ndipo ndakuchimwirani chiyani kuti muchite kundilondola mokwiya chonchi?
-