-
Genesis 31:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Popeza mwafufuza katundu wanga yense, kodi mwapezapo chiyani chamʼnyumba mwanu? Chiikeni apa pamaso pa abale anga ndi abale anu kuti atiweruze.
-