Genesis 31:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Sindinakubweretserenipo nyama iliyonse imene inaphedwa ndi chilombo+ koma ndinkaitenga kuti ikhale yanga. Nyama ikabedwa masana kapena usiku, munkandiuza kuti ndikulipireni.
39 Sindinakubweretserenipo nyama iliyonse imene inaphedwa ndi chilombo+ koma ndinkaitenga kuti ikhale yanga. Nyama ikabedwa masana kapena usiku, munkandiuza kuti ndikulipireni.