-
Genesis 31:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Ndiyeno Labani anamuyankha Yakobo kuti: “Akaziwa ndi ana anga, ana awo ndi ana anga, ziwetozi ndi ziweto zanga, ndipo chilichonse chimene ukuchiona ndi cha ine ndi ana anga aakaziwa. Ndiye kodi lero iwowa kapena ana awo amene anabereka, ndingawachitire choipa?
-