-
Genesis 31:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Kenako Yakobo anauza abale ake kuti: “Tengani miyala!” Iwo anatenga miyala nʼkuiunjika mulu. Atatero, anadyera chakudya pamulu wamiyalawo.
-