Genesis 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako Labani ananena kuti: “Mulu wamiyalawu ndi umboni wathu lero pakati pa ine ndi iwe.” Nʼchifukwa chake anaupatsa dzina lakuti Galeeda,+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:48 Utumiki Komanso Moyo Wathu,4/2020, tsa. 4
48 Kenako Labani ananena kuti: “Mulu wamiyalawu ndi umboni wathu lero pakati pa ine ndi iwe.” Nʼchifukwa chake anaupatsa dzina lakuti Galeeda,+