Genesis 31:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Ukamakazunza ana angawa ndiponso ukakatenga akazi ena kuwonjezera pa ana angawa, ngakhale kuti palibe munthu amene adzaone,* kumbukira kuti Mulungu ndi mboni pakati pa ine ndi iwe.”
50 Ukamakazunza ana angawa ndiponso ukakatenga akazi ena kuwonjezera pa ana angawa, ngakhale kuti palibe munthu amene adzaone,* kumbukira kuti Mulungu ndi mboni pakati pa ine ndi iwe.”