Genesis 31:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi umboni+ pakati pa ine ndi iwe, kuti wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake zoipa.
52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi umboni+ pakati pa ine ndi iwe, kuti wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake zoipa.