-
Genesis 31:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe mʼphirimo nʼkuitana abale ake kuti adye chakudya. Choncho iwo anadya chakudya nʼkugona mʼphirimo usiku umenewo.
-