Genesis 31:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Ndiyeno Labani anadzuka mʼmamawa nʼkukisa zidzukulu*+ zake ndi ana ake aakazi ndipo anawadalitsa.+ Atatero, ananyamuka nʼkubwerera kwawo.+
55 Ndiyeno Labani anadzuka mʼmamawa nʼkukisa zidzukulu*+ zake ndi ana ake aakazi ndipo anawadalitsa.+ Atatero, ananyamuka nʼkubwerera kwawo.+