-
Genesis 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Lero mukundithamangitsa pamalo ano ndipo sindidzathanso kukuyandikirani. Ndidzakhala woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi, ndipo aliyense wondipeza, ndithu adzandipha.”
-