Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!” Choncho malowo anawatchula kuti Mahanaimu.*