Genesis 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Choncho anagawa mʼmagulu awiri anthu amene anali nawo, nkhosa, mbuzi, ngʼombe ndi ngamila.
7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Choncho anagawa mʼmagulu awiri anthu amene anali nawo, nkhosa, mbuzi, ngʼombe ndi ngamila.