Genesis 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndine wosayenerera chikondi chokhulupirika komanso kukoma mtima konseku, kumene mwandisonyeza ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo pano ndili ndi magulu awiriwa.+
10 Ine ndine wosayenerera chikondi chokhulupirika komanso kukoma mtima konseku, kumene mwandisonyeza ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo pano ndili ndi magulu awiriwa.+