Genesis 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde ndipulumutseni+ mʼdzanja la mchimwene wanga, Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, akhoza kundivulaza+ komanso kuvulaza akaziwa limodzi ndi ana awo.
11 Chonde ndipulumutseni+ mʼdzanja la mchimwene wanga, Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, akhoza kundivulaza+ komanso kuvulaza akaziwa limodzi ndi ana awo.