Genesis 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yehova anauza Kaini kuti: “Chifukwa cha zimene wanenazi, aliyense amene adzaphe iweyo Kaini, adzalangidwa maulendo 7.” Choncho Yehova anaikira Kaini chizindikiro* kuti aliyense womupeza asamuphe. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,1/1/2004, tsa. 291/15/2002, ptsa. 22-232/1/1999, tsa. 21
15 Ndiyeno Yehova anauza Kaini kuti: “Chifukwa cha zimene wanenazi, aliyense amene adzaphe iweyo Kaini, adzalangidwa maulendo 7.” Choncho Yehova anaikira Kaini chizindikiro* kuti aliyense womupeza asamuphe.