Genesis 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu munanena kuti: ‘Ndithu ndidzakusamalira, ndipo ndidzachulukitsa mbadwa* zako ngati mchenga wakunyanja, womwe ndi wosawerengeka.’”+
12 Pajatu munanena kuti: ‘Ndithu ndidzakusamalira, ndipo ndidzachulukitsa mbadwa* zako ngati mchenga wakunyanja, womwe ndi wosawerengeka.’”+