-
Genesis 32:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako anapatsa anyamata ake magulu a ziwetozo, gulu lililonse palokha nʼkuwauza kuti: “Tsogolani muwoloke mtsinje, ndipo muzisiya mpata pakati pa gulu lililonse la ziweto.”
-