Genesis 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali mʼmbuyo mwathumu.’” Popeza mumtima mwake anati: “Ngati angasangalale ndi mphatso imene ndatumizayi,+ ndiye kuti ndikakumana naye akhoza kundilandira bwino.”
20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali mʼmbuyo mwathumu.’” Popeza mumtima mwake anati: “Ngati angasangalale ndi mphatso imene ndatumizayi,+ ndiye kuti ndikakumana naye akhoza kundilandira bwino.”