Genesis 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nayenso Yakobo anamuuza kuti: “Iwenso undiuze dzina lako.” Koma iye anati: “Nʼchifukwa chiyani ukufuna kudziwa dzina langa?”+ Atatero, anamudalitsa pamalo amenewo.
29 Nayenso Yakobo anamuuza kuti: “Iwenso undiuze dzina lako.” Koma iye anati: “Nʼchifukwa chiyani ukufuna kudziwa dzina langa?”+ Atatero, anamudalitsa pamalo amenewo.