Genesis 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Esau anathamanga kukakumana naye ndipo anamukumbatira nʼkumukisa.* Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri.
4 Koma Esau anathamanga kukakumana naye ndipo anamukumbatira nʼkumukisa.* Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri.