Genesis 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Yakobo anati: “Monga mukudziwa mbuyanga, anawa ndi osakhwima,+ komanso ndili ndi nkhosa ndi ngʼombe zoyamwitsa. Tikaziyendetsa mofulumira kwambiri kwa tsiku limodzi, ziweto zonse zifa.
13 Koma Yakobo anati: “Monga mukudziwa mbuyanga, anawa ndi osakhwima,+ komanso ndili ndi nkhosa ndi ngʼombe zoyamwitsa. Tikaziyendetsa mofulumira kwambiri kwa tsiku limodzi, ziweto zonse zifa.