Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sekemu mwana wamwamuna wa Hamori Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri amumzindawu ataona mtsikanayu, anamutenga nʼkumugwiririra. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:2 Mulungu Azikukondani, ptsa. 123-124 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 102-103
2 Ndiyeno Sekemu mwana wamwamuna wa Hamori Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri amumzindawu ataona mtsikanayu, anamutenga nʼkumugwiririra.