-
Genesis 34:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma ana a Yakobo atamva za nkhaniyi, nthawi yomweyo anabwerako koweta ziweto kuja. Nkhaniyi inawapweteketsa mtima kwambiri ndipo anakwiya koopsa, chifukwa Sekemu anachitira Isiraeli chinthu chochititsa manyazi kwambiri pogona ndi mwana wa Yakobo.+ Zimenezi zinali zosayenera kuchitika ngakhale pangʼono.+
-