Genesis 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwezani kwambiri ndalama za malowolo ndi mphatso zoti ndipereke.+ Ndine wokonzeka kupereka chilichonse chimene mungandiuze, bola mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.”
12 Kwezani kwambiri ndalama za malowolo ndi mphatso zoti ndipereke.+ Ndine wokonzeka kupereka chilichonse chimene mungandiuze, bola mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.”