Ekisodo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ndiyeno awa ndi mayina a ana a Isiraeli kapena kuti Yakobo, amene anapita nawo ku Iguputo. Mwana wamwamuna aliyense anapita limodzi ndi banja lake:+
1 Ndiyeno awa ndi mayina a ana a Isiraeli kapena kuti Yakobo, amene anapita nawo ku Iguputo. Mwana wamwamuna aliyense anapita limodzi ndi banja lake:+