Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana onse a Yakobo komanso zidzukulu zake* analipo 70, koma Yosefe anali kale ku Iguputo.+