Ekisodo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi Yosefe anamwalira,+ chimodzimodzinso abale ake onse ndi anthu a mʼbadwo wonsewo.