Ekisodo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aisiraeli* anaberekana ndipo anachuluka kwambiri mʼdzikomo. Iwo anapitiriza kukhala amphamvu komanso anachulukana mofulumira kwambiri, moti anadzaza mʼdzikomo.+
7 Aisiraeli* anaberekana ndipo anachuluka kwambiri mʼdzikomo. Iwo anapitiriza kukhala amphamvu komanso anachulukana mofulumira kwambiri, moti anadzaza mʼdzikomo.+