Ekisodo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamene ankawazunza kwambiri mʼpamenenso ankawonjezeka komanso kufalikira kwambiri, moti Aiguputo anachita mantha kwambiri chifukwa cha Aisiraeliwo.+
12 Koma pamene ankawazunza kwambiri mʼpamenenso ankawonjezeka komanso kufalikira kwambiri, moti Aiguputo anachita mantha kwambiri chifukwa cha Aisiraeliwo.+