Ekisodo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Aiguputo anakakamiza Aisiraeli kuti azigwira ntchito yaukapolo mwankhanza.+