Ekisodo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa, yomwe inali yoponda matope ndi kuumba njerwa. Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse mʼmunda. Ankawazunza komanso kuwagwiritsa ntchito ya mtundu uliwonse wa ukapolo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, ptsa. 24-256/15/2002, ptsa. 8-911/15/1987, ptsa. 30-31
14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa, yomwe inali yoponda matope ndi kuumba njerwa. Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse mʼmunda. Ankawazunza komanso kuwagwiritsa ntchito ya mtundu uliwonse wa ukapolo.+