Ekisodo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mfumu ya Iguputo inalankhula ndi azamba* a Chiheberi, amene mayina awo anali Sifira ndi Puwa.
15 Kenako mfumu ya Iguputo inalankhula ndi azamba* a Chiheberi, amene mayina awo anali Sifira ndi Puwa.