Ekisodo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma azambawo ankaopa Mulungu woona, ndipo sanachite zimene mfumu ya Iguputo inawauza. Mʼmalomwake, ana aamuna ankawasiya amoyo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Nsanja ya Olonda,11/1/2003, ptsa. 8-9
17 Koma azambawo ankaopa Mulungu woona, ndipo sanachite zimene mfumu ya Iguputo inawauza. Mʼmalomwake, ana aamuna ankawasiya amoyo.+