-
Ekisodo 1:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Azambawo anauza Farao kuti: “Akazi a Chiheberi sali ngati akazi a ku Iguputo kuno. Akazi a Chiheberi ndi amphamvu, moti mzamba asanafike iwo amakhala atabereka kale.”
-