Ekisodo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mkaziyo anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ataona kuti mwanayo ndi wokongola, anamubisa kwa miyezi itatu.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 30
2 Mkaziyo anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ataona kuti mwanayo ndi wokongola, anamubisa kwa miyezi itatu.+