Ekisodo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwanayo atafika poti sangathenso kumubisa,+ anatenga kabasiketi* kagumbwa* nʼkukamata phula. Kenako anaikamo mwanayo nʼkukasiya kabasiketiko pakati pa mabango mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,6/15/2002, tsa. 95/1/1997, tsa. 30
3 Mwanayo atafika poti sangathenso kumubisa,+ anatenga kabasiketi* kagumbwa* nʼkukamata phula. Kenako anaikamo mwanayo nʼkukasiya kabasiketiko pakati pa mabango mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo.