Ekisodo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wamkazi wa Farao atapita kukasamba mumtsinje wa Nailo, atsikana ake omutumikira ankayenda mʼmphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabasiketi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 30
5 Mwana wamkazi wa Farao atapita kukasamba mumtsinje wa Nailo, atsikana ake omutumikira ankayenda mʼmphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabasiketi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+