-
Ekisodo 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno mwana wa Farao anauza mayiyo kuti: “Tenga mwanayu ukandilerere ndipo ine ndizikulipira.” Choncho mayiyo anatenga mwanayo ndipo anamulera.
-