Ekisodo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 196/15/2002, tsa. 105/1/1997, tsa. 31 Galamukani!,4/8/2004, ptsa. 21-22
10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+
2:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 196/15/2002, tsa. 105/1/1997, tsa. 31 Galamukani!,4/8/2004, ptsa. 21-22