Ekisodo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano mʼmasiku amenewo, Mose atakula* anapita kwa abale ake kuti akaone mmene ankavutikira ndi ntchito yaukapolo+ imene ankagwira. Kumeneko anaona mʼbale wake wa Chiheberi akumenyedwa ndi nzika ina ya ku Iguputo.
11 Tsopano mʼmasiku amenewo, Mose atakula* anapita kwa abale ake kuti akaone mmene ankavutikira ndi ntchito yaukapolo+ imene ankagwira. Kumeneko anaona mʼbale wake wa Chiheberi akumenyedwa ndi nzika ina ya ku Iguputo.