Ekisodo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anayangʼana uku ndi uku ndipo ataona kuti palibe amene akumuona, anapha munthu wa ku Iguputoyo nʼkumubisa mumchenga.+
12 Choncho anayangʼana uku ndi uku ndipo ataona kuti palibe amene akumuona, anapha munthu wa ku Iguputoyo nʼkumubisa mumchenga.+