Ekisodo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma tsiku lotsatira atapitanso, anapeza amuna awiri a Chiheberi akumenyana. Choncho anafunsa wolakwayo kuti: “Ukumʼmenyeranji mnzako?”+
13 Koma tsiku lotsatira atapitanso, anapeza amuna awiri a Chiheberi akumenyana. Choncho anafunsa wolakwayo kuti: “Ukumʼmenyeranji mnzako?”+